LUKA 1
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU |Tengelani Kudzicepetsa kwa Mariya
Yehova anapatsa Mariya mwayi wapadela cifukwa anali na mtima wabwino.
1:38, 46-55
Kodi mau amene Mariya anakamba aonetsa bwanji kuti anali . . .
-
wodzicepetsa?
-
wa cikhulupililo colimba?
-
kuwadziŵa bwino Malemba?
-
munthu woyamikila?