June 4-10
MALIKO 15-16
Nyimbo 95 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Kukwanilitsidwa kwa Maulosi Okhudza Yesu”: (10 min.)
Maliko 15:3-5—Pamene Yesu anali kunenezedwa sanayankhe ciliconse
Maliko 15:24, 29, 30—Anthu anacita maele pa zovala zake, ndipo anamuzunza kwambili (“kugaŵana malaya ake akunja” “kupukusa mitu yawo” nwtsty mfundo zounikila pa Maliko 15:24, 29)
Maliko 15:43, 46—Iye anaikiwa m’manda a anthu olemela (“Yosefe” nwtsty mfundo younikila pa Maliko 15:43)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Maliko 15:25—N’cifukwa ciani nthawi imene Yesu anapacikiwa pa mtengo imaonetsedwa mosiyana? (“ca m’ma 9 koloko m’maŵa” nwtsty mfundo younikila)
Maliko 16:8—N’cifukwa ciani Baibulo la Dziko Latsopano lokonzedwanso ilibe mau omaliza aatali komanso mau omaliza aafupi mu Uthenga Wabwino wa Maliko? (“cifukwa anagwidwa ndi mantha” nwtsty mfundo younikila)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Maliko 15:1-15
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.
Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) jl phunzilo 2
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Tsatilani Mapazi a Khristu Mosamala Kwambili”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Dzina la Yehova N’lofunika Kwambili.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 23, na bokosi pa peji 60
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 140 na Pemphelo