Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Makambilano Acitsanzo

Makambilano Acitsanzo

●○○ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi tili m’masiku otsiliza?

Lemba: 2 Tim. 3:1-5

Ulalo: N’ciani cidzacitika pambuyo pa masiku otsiliza?

○●○ULENDO WOBWELELAKO WOYAMBA

Funso: N’ciani cidzacitika pambuyo pa masiku otsiliza?

Lemba: Chiv. 21:3, 4

Ulalo: Tingacite ciani kuti tikalandile madalitso amene Mulungu walonjeza kutsogolo?

○○●ULENDO WOBWELELAKO WACIŴILI

Funso: Tingacite ciani kuti tikalandile madalitso amene Mulungu walonjeza kutsogolo?

Lemba: Yoh. 3:16

Ulalo: Kodi kukhala na cikhulupililo kumatanthauza ciani?