AEFESO 4-6
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU |“Valani Zida Zonse Zankhondo Zocokela kwa Mulungu”
6:11-17
Mtumwi Paulo anayelekezela Akhristu na asilikali amene ali pa nkhondo. Adani athu ni “makamu a mizimu yoipa.” Koma olo tioneke ngati ofooka komanso osatetezeka, Yehova angatithandize kupambana pa nkhondoyi, malinga ngati tavala “zida zonse zankhondo zocokela kwa Mulungu.”
Chulani dzina la cida ciliconse ca nkhondo, na kufotokoza zimene cimaimila
ZOFUNIKA KUSINKHA-SINKHA: Kodi ndavala zida zonse za nkhondo?