June 24-30
AFILIPI 1-4
Nyimbo 33 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Musamade Nkhawa ndi Kanthu Kalikonse”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Afilipi.]
Afil. 4:6—Mukakhala na nkhawa cifukwa ca vuto linalake, pemphelo lingakuthandizeni (w17.08 10 ¶10)
Afil. 4:7—Lolani “mtendele wa Mulungu” kukutsogolelani (w17.08 10 ¶7; 12 ¶16)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Afil. 2:17—Kodi mtumwi Paulo anakhala “ngati nsembe yacakumwa imene ikuthilidwa” m’lingalilo lotani? (it-2 528 ¶5)
Afil. 3:11—Kodi “kuuka koyambilila” n’ciani? (w07 1/1 26-27 ¶5)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Afil. 4:10-23 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 4)
Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) fg phunzilo 6 ¶3-4 (th phunzilo 8)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Kodi Zipangizo Zanu Zimakulamulilani?: (5 min.) Tambitsani vidiyoyi. Pambuyo pake, yankhani mafunso aya: Kodi mafoni kapena matabuleti ni othandiza bwanji? Ni zotulukapo ziti zoipa zimene zimakhalapo ngati mukonda zipangizo zimenezi monyanya? Nanga mungadziŵe bwanji ngati mumakonda zipangizo zimenezi monyanya? Mungacite ciani kuti muzicita “zinthu zofunika kwambili”? (Afil. 1:10)
“Sankhani Zosangalatsa Mwanzelu”: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kodi Niyenela Kusankha Zosangalatsa Zabwanji?
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 72
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 76 na Pemphelo