UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO June 2020
Makambilano Acitsanzo
Mpambo wa makambilano onena za Yesu Khristu na nsembe yake.
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Yosefe Anakhululukila Abale Ake
Kodi tingaphunzile ciani kwa Yosefe pa nkhani yokhululukila ena?
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Thandizo la Cakudya pa Nthawi ya Njala
Ngakhale kuti anthu m’dzikoli ali na njala yauzimu, ni kuti kumene tingapeze cakudya cauzimu ca mwana alilenji?
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Acikulile Ali na Zambili Zotiphunzitsa
Kodi acikulile amapeleka citsanzo cotani cacikulupililo?
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Kodi Mungaphunzile Ciani kwa Akhristu Amene ni Aciyambakale?
Kodi mungapindule motani na zinthu zokondweletsa zimene aciyambakale anapeza pa utumiki wawo?
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Ndidzakhala Amene Ndidzafune Kukhala”
Kodi tanthauzo la dzina la Mulungu limakukhudzani bwanji?
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Ine Ndidzakhala Nawe Polankhula”
Kodi citsanzo ca Mose cingakulimbikitseni bwanji kuthetsa mantha polalikila?
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Moseŵenzetsela Makambilano Acitsanzo
Kodi tiyenela kuseŵenzetsa bwanji makambilano acitsanzo a m’kabuku ka misonkhano pokamba nkhani m’sukulu komanso mu ulaliki ministry?
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Mungakwanitse Kulalikila na Kuphunzitsa!
Kodi mungapeze kuti mphamvu na kulimba mtima kuti mukwanitse kulalikila na kuphunzitsa?