June 1-7
GENESIS 44-45
Nyimbo 130 na Pemphelo
Mawu Oyamba (1 min.)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yosefe Anakhululukila Abale Ake”: (10 min.)
Gen. 44:1, 2—Yosefe anayesa abale ake kuti aone ngati anasintha (w15 5/1 14-15)
Gen. 44:33, 34—Yuda anacondelela Yosefe kuti amasule Benjamini
Gen. 45:4, 5—Yosefe anatengela citsanzo ca Yehova pokhululukila abale ake
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)
Gen. 44:13—Kodi kung’amba covala kunali kutanthauza ciani? (it-2 813)
Gen. 45:5-8—N’ciani cingatithandize kupilila zinthu zopanda cilungamo? (w04 8/15 15 ¶15)
Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 45:1-15 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Nkhani Yophunzitsadi Kanthu Omvela, ndiyeno kambilanani phunzilo 18, m’bulosha ya Kuphunzitsa.
Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w06 2/1 31—Mutu: Kodi Yosefe pogwilitsila nchito kapu yapadela yasiliva anawombezadi maula, monga mmene zingaonekele pa Genesis 44:5, 15? (th phunzilo 18)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (10 min.)
Zimene Gulu Likukwanilitsa: (5 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya June.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 117
Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)
Nyimbo 19 na Pemphelo