March 28– April 3
Yobu 11-15
Nyimbo 111 ndi Pemphelo
Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Yobu Anali ndi Cidalilo Cakuti Akufa Adzauka”: (Mph. 10)
Yobu 14:1, 2—Yobu anafotokoza kutalika kwa moyo wa anthu (w15–CIN 3/1 3; w10 5/1 5 ndime 2; w08–CN 3/1 3 ndime 3)
Yobu 14:13-15a—Yobu anadziŵa kuti Yehova sadzamuiŵala (w15–E 8/1 5; w14 1/1 7 ndime 4; w11–CN 3/1 22 ndime 2-4)
Yobu 14:15b—Yehova amakonda atumiki ake okhulupilika (w15–E 8/1 7 ndime 3; w14–CN 6/15 14 ndime 12; w11–CN 3/1 22 ndime 3-6)
Kufufuza Cuma Cakuuzimu (Mph. 8)
Yobu 12:12—N’cifukwa ciani Akristu okalamba ndi oyenelela kuthandiza Akristu acinyamata? (g99 8/8 tsa.11, bokosi)
Yobu 15:27—Kodi Elifazi anatanthauza ciani pamene anakamba kuti nkhope ya Yobu “yaphimbika ndi mafuta a m’thupi mwake”? (it-1 E 802 ndime 4)
Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwandiphunzitsa ciani za Yehova?
Ndi mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingagwilitsile nchito mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibulo: Yobu 14:1-22 (Mph. 4 kapena zocepelapo)
KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI
Ulendo Woyamba: fg phunzilo 13 ndime 1. Yalani maziko a ulendo wobwelelako. (Mph. 2 kapena zocepelapo)
Ulendo Wobwelelako: fg phunzilo 13 ndime 2. Yalani maziko a ulendo wina wobwelelako. (Mph. 4 kapena zocepelapo)
Phunzilo la Baibulo: fg phunzilo 13 ndime 3-4 (Mph. 6 kapena zocepelapo)
UMOYO WATHU WACIKRISTU
Zosoŵa za pampingo (Mph. 5)
“Ciukililo Cidzatheka Kupitila mu Nsembe ya Dipo”: (Mph. 10) Kukambilana. Ngati n’zotheka tsilizani mwa kuonetsa vidiyo imene inaonetsedwa pa Msonkhano wa Cigawo wa mu 2014 wa mutu wakuti, “Pitilizani Kufunafuna Ufumu wa Mulungu Coyamba.”
Phunzilo la Baibulo la Mpingo: ia mutu 12 ndime 1-12 (Mph. 30)
Kubweleza Mfundo Zimene Taphunzila ndi Kufotokoza Zomwe Tidzaphunzila Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 33 ndi Pemphelo