Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YEREMIYA 8-11

Anthu Angapambane Kokha Ngati Atsogozedwa na Yehova

Anthu Angapambane Kokha Ngati Atsogozedwa na Yehova

Anthu sangakwanitse kudzilamulila, ndipo si oyenelela kutelo

10:21-23

  • Cifukwa cakuti abusa auzimu a Aisiraeli sanali kufunsila kwa Yehova, anthu anamwazikana

  • Koma amene anatsatila citsogozo ca Yehova anali kukhala mwa mtendele mwa cimwemwe, ndipo zinthu zinali kuwayendela bwino