Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YEREMIYA 1-4

“Ine Ndili ndi Iwe Kuti Ndikulanditse”

“Ine Ndili ndi Iwe Kuti Ndikulanditse”

Yeremiya ayenela kuti anali na zaka pafupi-fupi 25 pamene Yehova anamuika kukhala mneneli. Yeremiya anadziona kuti ni wosayenelela udindowo, koma Yehova anam’tsimikizila kuti adzapitiliza kum’thandiza.

  1. 647

    Yeremiya aikidwa kukhala mneneli

  2. 607

    Yerusalemu awonongedwa

  3. 580

    Atsiliza kulemba

Madeti onse ni a mu B.C.E.