Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU MATEYU 22-23

Muzitsatila Malamulo Aŵili Aakulu a m’Cilamulo

Muzitsatila Malamulo Aŵili Aakulu a m’Cilamulo

22:36-39

Mwa kuseŵenzetsa Mateyu 22:36-39, ikani namba kulingana na kufunika kwa cifukwa copitila ku misonkhano yacikhristu:

  • Kukalimbikitsidwa

  • Kukalimbikitsa abale athu

  • Kukalambila na kukaonetsa cikondi cathu pa Yehova

N’cifukwa ciani tiyenela kuyesetsa kupita ku misonkhano olo kuti talema, ndipo tiona monga sitidzapindula mokwanila na misonkhano?

Ni m’njila zina ziti zimene tingaonetsele kuti tikutsatila malamulo aŵili aakulu?