Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

March 5-​11

MATEYU 20-21

March 5-​11
  • Nyimbo 76 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Aliyense Wofuna Kukhala Wamkulu Pakati Panu Ayenela Kukhala Mtumiki Wanu”: (10 min.)

    • Mat. 20:3—Alembi na Afarisi onyada anali kukonda kuimilila pamsika kuti anthu awaone na kuwapatsa moni (“Pamsikanwtsty zithunzi)

    • Mat. 20:20, 21—Atumwi aŵili anapempha malo apamwamba ndi a ulamulilo (“mkazi wa Zebedayo” “mmodzi kudzanja lanu lamanja, wina kumanzele kwanuMat. 20:20, 21 nwtsty mfundo zounikila)

    • Mat. 20:25-28—Yesu anafotokoza kuti otsatila ake afunika kukhala atumiki odzicepetsa (“mtumiki” “sanabwele kudzatumikilidwa, koma kudzatumikilanwtsty mfundo zounikila pa Mat. 20:26, 28)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mat. 21:9—Kodi khamu la anthu linatanthauza ciani pamene linafuula kuti: “M’pulumutseni” “Mwana wa Davide!”? (nwtsty mfundo younikila)

    • Mat. 21:18, 19—N’cifukwa ciani Yesu anafotetsa mtengo wa mkuyu? (jy peji 244 mapa. 4-6)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mat. 20:1-19

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 99

  • Zofunikila za Mpingo: (5 min.)

  • Zimene Gulu Likukwanilitsa: (10 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya March.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy Mutu 11

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 53 na Pemphelo