Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MATEYU 24

Khalanibe Ogalamuka m’Masiku Otsiliza Ano

Khalanibe Ogalamuka m’Masiku Otsiliza Ano

24:39

Masiku ano, kufuna-funa zinthu za kuthupi kwacititsa anthu ambili kulephela kucita zinthu zauzimu. Kodi Akhristu ogalamuka mwauzimu amasiyana bwanji ndi anthu a ku dziko m’kaonedwe kawo pa nkhani ya . . .

  • maphunzilo apamwamba?

  • zosangalatsa?

  • nchito?

  • zinthu za kuthupi?