Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Tili ku Mapeto a Dongosolo Lino la Zinthu

Tili ku Mapeto a Dongosolo Lino la Zinthu

Tambani vidiyo yakuti Tili ku Mapeto a Dongosolo Lino la Zinthu, ndiyeno yankhani mafunso otsatilawa okhudzana na lemba la Mateyu 24:34.

  • Kodi mau akuti “zinthu zonsezi” atanthauza ciani?

  • Kodi lemba la Ekisodo 1:6 itithandiza bwanji kumvetsa tanthauzo la mau akuti “m’badwo”?

  • Ni m’badwo uti kweni-kweni umene Yesu anali kukambapo?

  • Ni magulu aŵili ati amene amapanga “m’badwo uwu”?

  • Kodi mau a Yesu aonetsa bwanji kuti tili mkati mweni-mweni mwa masiku otsiliza?