Akuseŵenzetsa kavidiyo pophunzitsa munthu Baibo ku South Africa

UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO March 2019

Makambilano Acitsanzo

Makambilano otsatizana-tsatizana ofotokoza colinga ca Mulungu kwa anthu.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Kuonetsa Cikondi Cacikhristu Kumatanthauza Ciani?

Wina akatilakwila, kodi cikondi cacikhristu cimatithandiza kucita ciani?

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yang’anani kwa Yehova Kuti Akuthandizeni Kupilila na Kukutonthozani

Kupitila m’Mawu ake, Yehova amatitonthoza na kutithandiza kupilila.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Ndimwe Munthu Wakuthupi Kapena Wauzimu?

Aliyense wa ife afunika kukulitsa uzimu wake na kupitiliza kukhala munthu wauzimu.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Kunola Luso Lathu Mu Ulaliki—Kulemba Bwino Makalata

Ni zinthu ziti zimene muyenela kukumbukila polembela kalata munthu amene simum’dziŵa?

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Kalata ya Citsanzo

Lembani kalata yanu mogwilizana n’colinga cake, komanso cikhalidwe ca kumaloko.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Cofufumitsa Cacing’ono Cimafufumitsa Mtanda Wonse”

Kodi kucotsa munthu mu mpingo kumaonetsa bwanji cikondi?

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Seŵenzetsani Mavidiyo Pophunzitsa Anthu Baibo

Kodi mavidiyo mumawaseŵenzetsa mokwanila pophunzitsa anthu amene mumaphunzila nawo Baibo?