Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

March 11-17

AROMA 15-16

March 11-17
  • Nyimbo 33 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Yang’anani kwa Yehova Kuti Akuthandizeni Kupilila na Kukutonthozani”: (10 min.)

    • Aroma 15:4—Ŵelengani Mawu a Mulungu kuti mupeze citonthozo (w17.07 14 ¶11)

    • Aroma 15:5—Pemphani Yehova kuti akuthandizeni kupilila na kukutonthozani (w16.04 14 ¶5)

    • Aroma 15:13—Yehova amatipatsa ciyembekezo (w14 6/15 14 ¶11)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Aroma 15:27—Kodi Akhristu a mitundu ina anali na ‘nkhongole’ kwa Akhristu a ku Yerusalemu m’lingalilo lotani? (w89 12/1 24 ¶3)

    • Aroma 16:25—Kodi “cinsinsi copatulika cimene cakhala cobisika kuyambila nthawi zakale” n’ciani? (it-1858 ¶5)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Aroma 15:1-16 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 129

  • Mmene Yehova ‘Amapatsila Mphamvu Zopilila na Kutonthoza’: (15 min.) Tambitsani vidiyo imeneyi. Ndiyeno kambilanani mafunso aya:

    • Kodi mwaphunzilapo ciani pa mfundo ya kulandila citonthozo?

    • Nanga mwaphunzilapo ciani pa mfundo ya kupeleka citonthozo?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 58

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 34 na Pemphelo