Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

March 18-24

1 AKORINTO 1-3

March 18-24
  • Nyimbo 127 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba. (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Kodi Ndimwe Munthu Wakuthupi Kapena Wauzimu?”: (10 min.)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • 1 Akor. 1:20—Kodi Mulungu anapanga bwanji “nzelu za dzikoli kukhala zopusa”? (it-2 1193 ¶1)

    • 1 Akor. 2:3-5—Kodi citsanzo ca Paulo cingatithandize bwanji? (w08 7/15 27 ¶6)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 1 Akor. 1:1-17 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 18

  • Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kulemba Bwino Makalata”: (8 min.) Kukambilana.

  • Kampeni Yomemeza Anthu ku Cikumbutso Idzayamba pa Ciŵelu, March 23: (7 min.) Nkhani yokambidwa na woyang’anila utumiki. Gaŵilani aliyense m’gulu kapepa koitanila anthu ku cikumbutso na kukambilana zimene zilimo. Tambitsani na kukambilana vidiyo ya ulaliki wacitsanzo. Fotokozani makonzedwe a mpingo wanu a mmene gawo lidzafoledwela.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 59

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 51 na Pemphelo