Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

March 4-10

AROMA 12-14

March 4-10
  • Nyimbo 106 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Kodi Kuonetsa Cikondi Cacikhristu Kumatanthauza Ciani?”: (10 min.)

    • Aroma 12:10—Tizikonda Akhristu anzathu (it-1 55)

    • Aroma 12:17-19—Munthu akatilakwila, tisamabwezele (w09 10/15 8 ¶3; w07 7/1 24-25 ¶12-13)

    • Aroma 12:20, 21—Gonjetsani coipa mwa kucita zinthu mokoma mtima (w12 11/15 29 ¶13)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Aroma 12:1—Kodi vesi iyi itanthauza ciani? (lvs 76-77 ¶5-6)

    • Aroma 13:1—Kodi olamulila akulu-akulu ali “m’malo awo osiyana-siyana mololedwa ndi Mulungu” m’lingalilo lotani? (w08 6/15 31 ¶4)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Aroma 13:1-14 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa: (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Gwilitsilani Nchito Mafunso, ndiyeno kambilanani phunzilo 3 m’bulosha ya Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (5 min. olo kucepelapo) w11 9/1 21-22—Mutu: N’cifukwa ciani Akhristu Afunika Kukhoma Misonkho ya Boma Olo Kuti Misonkhoyo Adzaiseŵenzetsa pa Zinthu Zosagwilizana na Malemba? (th phunzilo 3)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 77

  • Zofunikila za Mpingo: (15 min.)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 57

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 57 na Pemphelo