UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO March 2020
Makambilano Acitsanzo
Mpambo wa makambilano onena za Yesu Khristu na nsembe yake.
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mulungu . . . Anamuyesa Abulahamu”
N’cifukwa ciani Yehova anapempha Abulahamu kuti apeleke nsembe mwana wake?
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Mkazi wa Isaki
Kodi tingaphunzile ciani kwa mtumiki wa Abulahamu pamene tifuna kupanga zosankha zofunika?
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Kodi Nidzaitanila Ndani?
Ni anthu ena ati amene mungaitanile ku Cikumbutso ca imfa ya Khristu cimene cidzacitika posacedwapa?
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Esau Anagulitsa Udindo Wake Monga Woyamba Kubadwa
Ni zinthu zopatulika ziti zimene mufunika kuonetsa kuti mumaziyamikila?
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Yakobo Analandila Madalitso Omuyenelela
Kodi Yakobo analandila bwanji madalitso ake omuyenelela?
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Yakobo Akwatila
Kodi mungatani kuti mukhalebe na banja la cimwemwe olo mukumane na mavuto osayembekezela?
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kulalikila Anthu Akhungu
Kodi tingatengele bwanji citsanzo ca Yehova pa nkhani yosamalila ndiponso kukonda anthu akhungu m’gawo lathu?