Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 25-26

Esau Anagulitsa Udindo Wake Monga Woyamba Kubadwa

Esau Anagulitsa Udindo Wake Monga Woyamba Kubadwa

25:27-34

Esau ‘sanayamikile zinthu zopatulika.’ (Aheb. 12:16) Zotulukapo zake, anagulitsa udindo wake monga woyamba kubadwa. Anakwatilanso akazi aŵili amitundu ina.—Gen. 26:34, 35.

DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi ningaonetse bwanji kuti nimayamikila kwambili zinthu zopatulika izi?’

  • Ubale wanga na Yehova

  • Mzimu woyela

  • Kudziŵika na dzina loyela la Yehova

  • Ulaliki

  • Misonkhano yacikhristu

  • Cikwati