Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

March 2-8

GENESIS 22-23

March 2-8
  •  Nyimbo 89 na Pemphelo

  •  Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Mulungu . . . Anamuyesa Abulahamu”: (10 min.)

    • Gen. 22:1, 2—Mulungu anauza Abulahamu kuti apeleke nsembe Isaki mwana wake wokondedwa (w12 1/1 23 ¶4-6)

    • Gen. 22:9-12—Yehova anauza Abulahamu kuti asamuphe Isaki

    • Gen. 22:15-18—Yehova analonjeza Abulahamu kuti adzamudalitsa cifukwa cokhala womvela (w12 10/15 23 ¶6)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Gen. 22:5—N’cifukwa ciani Abulahamu anauza anyamata ake kuti iye na Isaki adzaŵapeza ngakhale kuti Abulahamuyo anali kudziŵa kuti akukam’peleka nsembe Isaki? (w16.02 11 ¶13)

    • Gen. 22:12—Kodi lembali lionetsa bwanji kuti Yehova amacita kusankha kuseŵenzetsa nzelu zake zodziŵilatu za kutsogolo? (it-1 853 ¶5-6)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mbali ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 22:1-18 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 4

  • Kumvela Kumatiteteza: (15 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Msonkhano wa Pacaka wa 2017—Nkhani na Lemba la Caka ca 2018—Kambali Kake.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 106

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 16 na Pemphelo