Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 24

Mkazi wa Isaki

Mkazi wa Isaki

24:2-4, 11-15, 58, 67

Mtumiki wa Abulahamu anapempha Yehova kuti amuthandize kusankha mkazi wa Isaki. (Gen. 24:42-44) Na ife tifunika kupempha citsogozo ca Yehova tisanapange zosankha zikulu-zikulu. Motani?

  • Pemphelani

  • Fufuzani m’Mawu a Mulungu na m’zofalitsa zathu

  • Pemphani thandizo kwa Akhristu ofikapo kuuzimu