April 26–May 2
NUMERI 25–26
Nyimbo 135 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Zocita za Munthu Mmodzi Zingapindulitse Ambili?”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu (Mph. 10)
Num. 26:55, 56—Kodi Yehova anaonetsa bwanji nzelu pogaŵa malo a colowa kwa mafuko a Aisiraeli? (it-1 359 ¶1-2)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 25:1-18 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Seŵenzetsani Makambilano Acitsanzo. (th phunzilo 1)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Chulani na kukambilana vidiyo imene mwasankha (koma musaitambitse). (th phunzilo 3)
Nkhani: (Mph. 5) w04 4/1 29—Mutu: N’cifukwa ciani ciŵelengelo ca anthu cochulidwa pa Numeri 25:9 n’cosiyana na ca pa 1 Akorinto 10:8? (th phunzilo 17)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Sankhani Mabwenzi Mwanzelu”: (Mph 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Zitsanzo Zoticenjeza Masiku Ano—Kambali Kake. Limbikitsani onse kuti akaonelele vidiyo yonse.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 34
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 126 na Pemphelo