April 5-11
NUMERI 17-19
Nyimbo 80 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Ine Ndine . . . Colowa Cako”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Num. 18:19, mawu amunsi—Kodi mawu akuti “pangano la mcele” atanthauza ciani? (g02 6/8 14 ¶2)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 18:1-13 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Yesu—Mat. 20:28. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela pasikilini.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 6)
Nkhani: (Mph. 5) w18.01 18 ¶4-6—Mutu: N’cifukwa Ciani Timapeleka Cuma Cathu kwa Yehova? (th phunzilo 20)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo (Mph. 15)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 30
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 8 na Pemphelo