Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mmene Cikhulupililo Cimatithandizila Kukhala Olimba Mtima

Mmene Cikhulupililo Cimatithandizila Kukhala Olimba Mtima

Azondi amene anabweletsa uthenga wofooketsa analibe cikhulupililo (Num. 13:31-33; 14:11)

Kusoŵa cikhulupililo kwa azondi 10 kunapangitsa abale awo kutaya mtima (Num. 14:1-4)

Azondi amene anakhalabe olimba mtima anali na cikhulupililo colimba (Num. 14:6-9; w06 10/1 16-17 ¶5-6)

Aisiraeli anali ataonapo kale nchito zopulumutsa za Yehova. Izi zinayenela kulimbitsa cikhulupililo cawo cakuti iye adzawathandiza kulanda dziko la Kanani.