Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Samalani na Kunyada Komanso Kudzidalila

Samalani na Kunyada Komanso Kudzidalila

Kora anapandukila makonzedwe a Yehova cifukwa anali wonyada komanso wodzidalila (Num. 16:1-3; w11 9/15 27 ¶12)

Kora anali Mlevi wolemekezeka ndipo anali na mautumiki ambili apadela (Num. 16:8-10; w11 9/15 27 ¶11)

Maganizo olakwika a Kora anabweletsa mavuto aakulu (Num. 16:32, 35)

Tisalole zinthu zimene tacita mu utumiki wa Yehova kutipangitsa kukhala wonyada na wodzidalila. Ngati takhala zaka zambili m’coonadi kapena ngati tili na maudindo aakulu, m’pamenenso tifunika kukhala odzicepetsa kwambili.