Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

March 14-20

1 SAMUELI 14-15

March 14-20

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Kumvela Kumaposa Nsembe”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Sam. 15:24—Kodi pali cenjezo lotani pa cifundo cosayenela cimene Sauli anaonetsa? (it-1 493)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 15:1-16 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 61

  • Kumemeza Anthu ku Cikumbutso Kudzayamba pa Ciŵelu, pa March 19: (Mph. 10) Kukambilana. Mwacidule, kambilanani zimene zili m’kapepala koitanila anthu ku Cikumbutso. Fotokozani makonzedwe a pampingo panu okhudza nkhani yapadela na Cikumbutso, komanso a mofolela magawo. Tambitsani na kukambilana vidiyo ya ulaliki wacitsanzo.

  • Khala Bwenzi la Yehova—Mvela Yehova: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 81

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 125 na Pemphelo