Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

March 21-27

1 SAMUELI 16-17

March 21-27
  • Nyimbo 7 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Yehova Ndiye Mwini Nkhondo”: (10 min.)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Sam. 16:14, na mawu a m’munsi.—Kodi mawu akuti Sauli analandila “mzimu woipa wocokela kwa Yehova” atanthauza ciani? (it-2 871-872)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 16:1-13 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kumemeza Anthu ku Cikumbutso: (Mph. 2) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 11)

  • Kumemeza Anthu ku Cikumbutso: (Mph. 3) Itanilani mnzanu wa kunchito, wa kusukulu, kapena wacibale amene munamulalikilapo kale. (th phunzilo 2)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Citani ulendo wobwelelako kwa munthu amene analandila kapepala koitanila anthu ku Cikumbutso, amenenso anaonetsa cidwi. (th phunzilo 4)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Citani ulendo wobwelelako kwa munthu amene analandila kapepala koitanila anthu ku Cikumbutso, amenenso anaonetsa cidwi. M’fotokozeleni za webusaiti yathu munthuyo. (th phunzilo 20)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU