March 28–April 3
1 SAMUELI 18-19
Nyimbo 36 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Khalanibe Odzicepetsa Zinthu Zikakuyendelani Bwino”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Sam. 19:23, 24—Kodi Mfumu Sauli anacita bwanji zinthu “ngati mneneli”? (it-2 695-696)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 18:25–19:7 (th phunzilo 11)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
“Wonjezelani Cimwemwe Canu mu Ulaliki—Thandizani Maphunzilo a Baibo Kuleka Makhalidwe Odetsa”: (Mph. 10) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Thandizani Maphunzilo Anu a Baibo Kuleka Makhalidwe Odetsa.
Nkhani: (Mph. 5) km 1/03 1—Mutu: Nchito Imene Imafuna Kudzicepetsa. (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 83
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 125 na Pemphelo