March 7-13
1 SAMUELI 12-13
Nyimbo 4 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kudzikweza Kumanyazitsa Munthu”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Sam. 12:21—Kodi Aisiraeli akanatsatila bwanji “milungu yopanda pake” (kapena kuti “zinthu zacabe” BL.)? (w11 7/15 13 ¶15)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 12:1-11 (th phunzilo 2)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Yesu—Mat. 16:16. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela mu vidiyo.
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 1)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 04 ndime yoyamba, na mfundo 1-2 (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zimene Gulu Likukwanilitsa: (Mph. 5) Onetsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya March.
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 10)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 80
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 69 na Pemphelo