Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

April 17-23

2 MBIRI 10-12

April 17-23

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Pindulani na Ulangizi Wanzelu”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Mbiri 11:15—Kodi mawu akuti “ziwanda zooneka ngati mbuzi” mwina anali kutanthauza ciyani? (it-1 966-967)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 10:1-15 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 12)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 6)

  • Nkhani: (Mph. 5) be 69 ¶4-5—Mutu: Phunzitsani Ophunzila Anu Mopangila Zisankho Akapempha Malangizo (th phunzilo 20)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU