April 24-30
2 MBIRI 13-16
Nyimbo 3 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Ni Nthawi Iti Pamene Tiyenela Kudalila Yehova?”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
2 Mbiri 15:16—Tingatengele bwanji kulimba mtima kwa Asa? (w17.03 19 ¶7)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 14:1-15 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za webusaiti yathu na kumusiyila kakhadi koloŵela pa jw.org. (th phunzilo 1)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za pulogilamu yathu yophunzitsa Baibo na kumusiyila kakhadi kopemphela Phunzilo la Baibo. (th phunzilo 11)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 09 mfundo 7 na mbali yakuti Anthu Ena Amakamba Kuti (th phunzilo 6)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Zisankho Zimene Zimaonetsa Kuti Timadalila Yehova”: (Mph. 15) Kukambilana komanso kutamba vidiyo.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 44 mfundo 1-4, na mfundo ya kumapeto 5
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 39 na Pemphelo