Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

March 6-12

1 MBIRI 23-26

March 6-12

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Kulambila pa Kacisi Kunayamba Kucitika Mwadongosolo Kwambili”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Mbiri 25:7, 8—Kodi mavesi amenewa aonetsa bwanji kufunika koimba nyimbo zotamanda Yehova? (w22.03 22 ¶10)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Mbiri 23:21-32 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 101

  • Mmene Tingathandizile Pakagwa Tsoka”: (Mph. 10) Kukambilana komanso kutamba vidiyo.

  • Kuitanila Anthu ku Cikumbutso Kudzayamba pa Ciŵelu, pa March 11: (Mph. 5) Kukambilana. Mwacidule kambilanani zimene zili m’kapepala koitanila anthu ku Cikumbutso. Fotokozani makonzedwe a pampingo panu okhudza nkhani yapadela na Cikumbutso, komanso mofolela magawo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 39 komanso mfundo ya kumapeto 3

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 127 na Pemphelo