April 15-21
MASALIMO 29-31
Nyimbo 108 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
1. Cilango ni Njila Imene Mulungu Amationetsela Cikondi
(Mph. 10)
Yehova anabisa nkhope yake pamene Davide sanamumvele (Sal. 30:7; it-1 802 ¶3)
Davide anapempha Yehova kuti amucitile cifundo (Sal. 30:8)
Yehova anamukhululukila Davide (Sal. 30:5; w07 3/1 19 ¶1)
Salimo 30 iyenela kuti imakamba zimene zinacitika Davide ataŵelenga anthu mu Isiraeli.—2 Sam. 24:25.
ZOFUNIKA KUZISINKHASINKHA: Kodi munthu wocotsedwa angapindule bwanji na cilango cimeneco? Nanga angaonetse bwanji kuti analapa zenizeni?—w21.10 6 ¶18.
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Sal. 31:23—Kodi munthu wodzikuza amalangidwa bwanji na Yehova mowilikiza? (w06 5/15 19 ¶12)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo ziti zothandiza zimene mungakonde kutigaŵilako?
3. Kuŵelenga Baibo
(Mph. 4) Sal. 31:1-24 (th phunzilo 10)
4. Kuyambitsa Makambilano
(Mph. 1) ULALIKI WAPOYELA. Mwacidule lalikilani munthu wotangwanika. (lmd phunzilo 5 mfundo 3)
5. Kuyambitsa Makambilano
(Mph. 3) ULALIKI WAMWAYI. Onetsani mayi vidiyo ya ana, ndipo m’fotokozeleni mmene angapezele mavidiyo ena. (lmd phunzilo 3 mfundo 3)
6. Kubwelelako
(Mph. 3) ULALIKI WAPOYELA. Yambitsani phunzilo la Baibo kwa munthu amene m’mbuyomu anakana kuphunzila. (lmd phunzilo 8 mfundo 3)
7. Kupanga Ophunzila
(Mph. 4) lff phunzilo 14 mfundo 5 (th phunzilo 6)
Nyimbo 45
8. Cifukwa Cake Timakhulupilila . . . Cikondi ca Mulungu
(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO. Kenako funsani omvela kuti:
Kodi vidiyo iyi yatiphunzitsa ciyani za cikondi ca Mulungu?
9. Ciunikilo ca 2024 ca Dipatimenti ya Mapulani na Mamangidwe
(Mph. 8) Nkhani. Tambitsani VIDIYO.
10. Phunzilo la Baibo la Mpingo
(Mph. 30) bt mutu 8 ¶13-21