Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

March 11-17

SALIMO 18

March 11-17

Nyimbo 148 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. “Yehova Ndiye . . . Wopeleka Cipulumutso kwa Ine”

(Mph. 10)

Yehova ali monga thanthwe, malo a citetezo, komanso cishango (Sal. 18:1, 2; w09 5/1 14 ¶4-5)

Yehova amamva kulila kwathu kopempha thandizo (Sal. 18:6; it-2 1161 ¶7)

Yehova amacitapo kanthu kuti atithandize (Sal. 18:​16, 17; w22.04 3 ¶1)

Yehova angaticotsele mavuto amene timakumana nawo mmene nthawi zina anali kucitila kwa Davide. Koma nthawi zambili Mulungu amapeleka njila yopulumukila potipatsa mphamvu kuti tikwanitse kuwapilila mavutowo.—1 Akor. 10:13.

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 18:10—N’cifukwa ciyani wamasalimo anakamba kuti Yehova wakwela pakerubi? (it-1 432 ¶2)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutigaŵilako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4) Sal. 18:20-39 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kukoma Mtima—Mmene Yesu Anaonetsela Khalidwe Limeneli

(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO, kenaka kambilanani lmd phunzilo 3 mfundo 1-2.

5. Kukoma Mtima—Tengelani Citsanzo ca Yesu

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 60

6. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 5)

7. Vidiyo ya Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita ya March

(Mph. 10) Tambitsani VIDIYO.

8. Phunzilo la Baibo la Mpingo

Mawu Othela (Mph. 3) | Nyimbo 69 na Pemphelo