March 18-24
MASALIMO 19-21
Nyimbo 6 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
1. “Zakumwamba Zikulengeza Ulemelelo wa Mulungu”
(Mph. 10)
Cilengedwe ca Yehova cimalengeza ulemelelo wake (Sal. 19:1; w04 1/1 8 ¶1-2)
Dzuŵa n’colengedwa codabwitsa (Sal. 19:4-6; w04 6/1 11 ¶8-10)
Tiyenela kuphunzila ku zinthu zimene Mulungu analenga (Mat. 6:28; g95 11/8 7 ¶3)
ZIMENE MUNGACITE PA KULAMBILA KWA PABANJA: Yang’anani zacilengedwe, kenaka kambilanani zimene mwaphunzilapo ponena za Yehova.
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Sal. 19:7-9—Kodi mavesiwa aonetsa bwanji kalembedwe kaluso kandakatulo m’Ciheberi? (it-1 1073)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutigaŵilako?
3. Kuŵelenga Baibo
(Mph. 4) Sal. 19:1-14 (th phunzilo 11)
4. Kuyambitsa Makambilano
(Mph. 3) ULALIKI WAPOYELA Gaŵilani munthu kapepala komuitanila ku Cikumbutso, ndipo gwilitsani nchito jw.org kuti mupeze malo a Cikumbutso kufupi na kwawo. (lmd phunzilo 2 mfundo 3)
5. Kuyambitsa Makambilano
(Mph. 4) ULALIKI WAMWAYI. Landilani munthu amene wabwela ku Cikumbutso cifukwa copeza kapepala ka ciitano pa khomo pake. Panganani zakuti mukayankhe mafunso amene ali nawo. (lmd phunzilo 3 mfundo 4)
6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupilila
(Mph. 5) Nkhani. ijwfq 45—Mutu: N’cifukwa Ciyani a Mboni za Yehova Mumacita Mwambo wa Mgonelo wa Ambuye Mosiyana na Zipembedzo Zina? (th phunzilo 6)
Nyimbo 141
7. Yang’anani Cilengedwe Kuti Mulimbitse Cikhulupililo Canu
(Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO. Kenako funsani omvela kuti:
Kodi zinthu zosiyana-siyana zacilengedwe zimalimbikitsa bwanji cikhulupililo canu mwa Mlengi?
8. Phunzilo la Baibo la Mpingo
(Mph. 30) bt mutu. 7 ¶9-13, bokosi pa tsa. 56