Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

March 25-31

SALIMO 22

March 25-31

Nyimbo 19 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Asilikali akucita maele pa zovala za Yesu

1. Baibo Inakambilatu Zodzacitika pa Imfa ya Yesu

(Mph. 10)

Yesu adzaoneka ngati Mulungu wamusiya (Sal. 22:1; w11 8/15 15 ¶16)

Yesu adzanyozedwa (Sal. 22:7, 8; w11 8/15 15 ¶13)

Anthu adzacita maele pa zovala za Yesu (Sal. 22:18; w11 8/15 15 ¶14; onani cithunzi pacikuto)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi Salimo 22 imalimbikitsa bwanji cikhulupililo canga kuti maulosi ena okamba za Mesiya nawonso adzakwanilitsika, monga wopezeka pa Mika 4:4?’

2. Kufufuza Cuma Cauzimu

(Mph. 10)

  • Sal. 22:22—Kodi masiku ano tingatengele citsanzo ca wamasalimo m’njila ziŵili ziti? (w06 11/1 29 ¶7; w03 9/1 20 ¶1)

  • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutigaŵilako?

3. Kuŵelenga Baibo

(Mph. 4.) Sal. 22:1-19 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

4. Kuyambitsa Makambilano

(Mph. 3) KUNYUMBA NA NYUMBA. (lmd phunzilo 4 mfundo 4)

5. Kubwelelako

(Mph. 4) ULALIKI WAMWAYI. Pangani ulendo wobwelelako kwa mnzanu amene anavomela kukapezekapo pa Cikumbutso. (lmd phunzilo 4 mfundo 3)

6. Nkhani

(Mph. 5) w20.07 12-13 ¶14-17—Mutu: Mmene Maulosi a m’Baibo Amalimbikitsila Cikhulupililo Cathu. (th phunzilo 20)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Nyimbo 95

7. Zofunikila za Mpingo

(Mph. 15)

8. Phunzilo la Baibo la Mpingo

Mawu Othela (3 min.) | Nyimbo 53 na Pemphelo