April 21-27
MIYAMBO 10
Nyimbo 76 ndi Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
1. Tingatani Kuti Tikhale Ndi Cimwemwe Ceniceni?
(Mph. 10)
Timakhala ndi umoyo wacimwemwe tikamagwila nchito mwakhama pothandiza anthu ena kudziwa Yehova (Miy. 10:4, 5; w01-CN 7/15 25 ¶1-3)
Kukhala wolungama n’kofunika kwambili kuposa kukhala ndi cuma (Miy. 10:15, 16; w01-CN 9/15 24 ¶3-4)
Madalitso a Yehova ndi amene amapangitsa munthu kukhala ndi cimwemwe ceniceni (Miy. 10:22; it-1-E 340)
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
-
Miy. 10:22—Popeza madalitso a Yehova sawonjezelapo ululu, n’cifukwa ciyani atumiki a Yehova amakumana ndi mavuto ambili? (w06-CN 5/15 30 ¶18)
-
Pa kuwelenga Baibulo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?
3. Kuwelenga Baibulo
(Mph. 4) Miy. 10:1-19 (th phunzilo 10)
4. Kuyambitsa Makambilano
(Mph. 4) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Munthuyo wakuuzani kuti sakhulupilila kuti kuli Mulungu. (lmd phunzilo 4 mfundo 3)
5. Kuyambitsa Makambilano
(Mph. 4) ULALIKI WAMWAYI. M’pempheni kuti muziphunzila naye Baibulo. (lmd phunzilo 4 mfundo 4)
6. Kubwelelako
(Mph. 4) ULALIKI WAMWAYI. Muonetseni mopezela nkhani imene ingamucititse cidwi pa jw.org. (lmd phunzilo 9 mfundo 4)
Nyimbo 111
7. Kodi Ndi Madalitso Ati Amene Amalemeletsa Atumiki a Mulungu?
(Mph. 7) Kukambilana.
Madalitso amene Yehova amapeleka kwa atumiki ake m’nthawi ino yovuta ya masiku otsiliza, amatithandiza kupilila komanso kukhala ndi umoyo wacimwemwe. (Sal. 4:3; Miy. 10:22) Welengani malemba amene ali pansipa. Kenako funsani omvela mmene dalitso lililonse limatithandizila kukhala acimwemwe.
-
Yes. 65:13
-
Luka 11:13
-
Yoh. 13:35
Ena akwanitsa kufutukula utumiki wawo ndipo akhala ndi umoyo wacimwemwe potumikila Yehova.
Tambitsani VIDIYO YAKUTI Inu Acinyamata—Sankhani Njila Yobweletsa Mtendele! Kenako funsani omvela kuti:
-
Kodi mwaphunzila ciyani kwa Harley, Anjil, ndi Carlee?
8. Lipoti la Dipatimenti Yoona za Mapulani ndi Zomangamanga la 2025
(Mph. 8) Nkhani. Tambitsani VIDIYO.
9. Phunzilo la Baibulo la Mpingo
(Mph. 30) bt mutu 25 ¶8-13, bokosi pa tsa. 201