March 31–April 6
MIYAMBO 7
Nyimbo 34 ndi Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
1. Pewani Zinthu Zimene Zingakugwetseleni M’mayeselo
(Mph. 10)
Mnyamata wosadziwa zinthu wasankha kupita ku malo kumene kumadziwika kuti kumapezeka anthu aciwelewele (Miy. 7:7-9; w00-CN 11/15 29 ¶5)
Mkazi amene ndi hule akumunyengelela kuti agone naye (Miy. 7:10, 13-21; w00-CN 11/15 30 ¶4-6)
Akukumana ndi mavuto cifukwa codzigwetsela m’mayeselo (Miy. 7:22, 23; w00-CN 11/15 31 ¶2)
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Miy. 7:3—Kodi kumanga malamulo a Mulungu ku zala zathu ndi kuwalemba pa mtima pathu kutanthauza ciyani?(w00-CN 11/15 29 ¶1)
Pa kuwelenga Baibulo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?
3. Kuwelenga Baibulo
(Mph. 4) Miy. 7:6-20 (th phunzilo 2)
4. Kubwelelako
(Mph. 4) KUNYUMBA NDI NYUMBA. Pa ulendo wapita, munthuyo analandila kapepala komuitanila ku Cikumbutso ndipo anaonetsa cidwi. (lmd phunzilo 9 mfundo 5)
5. Kubwelelako
(Mph. 4) ULALIKI WAMWAYI. Pa makambilano apita, munthuyo analandila kapepala komuitanila ku Cikumbutso ndipo anaonetsa cidwi. (lmd phunzilo 9 mfundo 4)
6. Kubwelelako
(Mph. 4) ULALIKI WAPOYELA. Pa makambilano apita, munthuyo analandila kapepala komuitanila ku Cikumbutso ndipo anaonetsa cidwi. (lmd phunzilo 9 mfundo 3)
Nyimbo 13
7. Nthawi Ina Yabwino (Luka 4:6)
(Mph. 15) Kukambilana.
Tambitsani VIDIYO Kenako funsani omvela kuti:
Kodi Yesu anayesedwa motani? Nanga ifeyo tingayesedwe bwanji m’njila yofananayo?
Kodi tingatani kuti tisagonje ku mayeselo a Mdyelekezi?
8. Phunzilo la Baibulo la Mpingo
(Mph. 30) bt mutu 24 ¶13-21