UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO May 2016
Maulaliki Acitsanzo
Maulaliki acitsanzo ogaŵila Nsanja ya Mlonda ndi buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa. Seŵenzetsani maulaliki acitsanzo amenewa kuti mukonze ulaliki wanu.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Yehova Amakondwela Tikamapemphelela Ena
Mulungu anauza Yobu kupemphelela anzake atatu opanda cifundo. Kodi Yobu anadalitsidwa bwanji kaamba ka cikhulupililo cake ndi kupilila? (Yobu 38-
UMOYO WATHU WACIKRISTU
Kodi Mukugwilitsila Nchito JW Laibulale?
Kodi mungaike bwanji JW Laibulale pa cipangizo canu? Kodi ingakuthandizeni bwanji pa misonkhano yampingo ndi mu ulaliki?
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Kuti Tikhale Pamtendele ndi Yehova, Tifunika Kulemekeza Mwana Wake, Yesu
Kodi anthu a mitundu ina acita bwanji ndi ulamulilo wa Yesu? N’cifukwa ciani tifunika kulemekeza Mfumu yodzozedwa ndi Mulungu? (Salimo 2)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Ndani Amene Angakhale Mlendo m’Cihema ca Yehova?
Lemba la Salimo 15 limafotokoza zimene Yehova amafuna mwa bwenzi lake.
UMOYO WATHU WACIKRISTU
Mmene Tingaseŵenzetsele JW Laibulale
Mmene mungaseŵenzetsele JW Laibulale pophunzila panokha, pa misonkhano, ndi mu ulaliki.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Maulosi Amatiuza Zambili Zokhudza Mesiya
Onani mmene maulosi okhudza Mesiya a m’buku la Salimo 22 anakwanilitsidwa pa Yesu.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Dalilani Yehova Kuti Akulimbitseni Mtima
N’ciani cingatithandize kukhala wolimba mtima monga Davide? (Salimo 27)