Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YOBU 38-42

Yehova Amakondwela Tikamapemphelela Ena

Yehova Amakondwela Tikamapemphelela Ena

Yehova anafuna kuti Yobu apemphelele Elifazi, Bilidadi, ndi Zofari

42:7-10

  • Yehova anauza Elifazi, Bilidadi ndi Zofari kuti apeleke nsembe yopseleza

  • Yobu anali kufunika kupemphelela anzake atatu

  • Yobu anadalitsidwa atapemphelela anzakewo

Yehova anadalitsa Yobu kwambili cifukwa ca cikhulupilililo cake ndi kupilila

42:10-17

  • Yehova anathetsa mavuto a Yobu, ndipo anamucilitsa matenda ake

  • Yobu anatonthozedwa ndi anzake komanso acibale ake pa mavuto amene anakumana nao

  • Yehova anabwezeletsa cuma cimene Yobu anali naco kuwilikiza kaŵili

  • Yobu ndi mkazi wake anakhalanso ndi ana ena 10

  • Yobu anakhala ndi moyo zaka zina 140, ndipo anali ndi mwai woona mbadwo wacinai wa mzele wake wobadwila