May 23- 29
SALIMO 19-25
Nyimbo 116 ndi Pemphelo
Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Maulosi Amatiuza Zambili Zokhudza Mesiya”: (Mph. 10)
Sal 22:1—Mesiya anaoneka ngati wasiidwa ndi Mulungu (w11-CN 8/15 15 ndime 16)
Sal 22:7, 8—Mesiya adzanyozedwa (w11-CN 8/15 15 ndime 13)
Sal 22:18—Adzacita maele pazovala za Mesiya (w11-CN 8/15 15 ndime 14)
Kufufuza Cuma Cakuuzimu: (Mph. 8)
Sal 19:14—Kodi tingaphunzilepo ciani pa vesi limeneli? (w06-CN 5/15 19 ndime 8)
Sal 23:1, 2—Kodi Yehova ndi M’busa wabwino motani? (w02-CN 9/15 32 ndime 1-2)
Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwandiphunzitsa ciani za Yehova?
Ndi mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingagwilitsile nchito mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Salimo 25:1-22
KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) bh—Ŵelengani lemba pa cipangizo cokhala ndi intaneti.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) bh—Seŵenzetsani JW Laibulale pofufuza, kuti mupeze vesi la m’Baibulo limene liyankha funso limene mwininyumba wafunsa.
Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) bh 129-130 ndime 11-12—Citani citsanzo cacidule coonetsa wofalitsa akuonetsa wophunzila Baibulo mmene angagwilitsile nchito JW Laibulale pokonzekela phunzilo pa cipangizo cokhala ndi intaneti.
UMOYO WATHU WACIKRISTU
“Mmene Tingaseŵenzetsele JW Laibulale”—Mbali 2: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani mavidiyo akuti Download and Manage Bibles ndi Search in a Bible or Publication ngati alipo. Ndiyeno kambilanani kamutu kothela pa nkhani imene mukukambilana. Pemphani omvela kuti akambe mmene anagwilitsila nchito JW Laibulale mu ulaliki.
Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu 16 ndime 1-15
Kubweleza Mfundo Zimene Taphunzila ndi Kufotokoza Zomwe Tidzaphunzila Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 139 ndi Pemphelo