May 30– June 5
SALIMO 26-33
Nyimbo 23 ndi Pemphelo
Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Dalilani Yehova Kuti Akulimbitseni Mtima”: (Mph. 10)
Sal. 27:1-3—Kuganizila mmene Yehova wakhalila kuwala kwathu kungatithandize kukhala wolimba mtima (w12-CN 7/15 22-23 ndime 3-6)
Sal. 27:4—Kukonda kulambila koona kumatithandiza kukhala wolimba mtima. (w12-CN 7/15 24 ndime 7)
Sal. 27:10—Yehova ndi wokonzeka kuthandiza atumiki ake pamene ena awasala. (w12-CN 7/15 24 ndime 9-10)
Kufufuza Cuma Cakuuzimu: (Mph. 8)
Sal. 26:6—Mofanana ndi Davide, kodi tingazungulile motani guwa la nsembe la Yehova? (w06-CN 5/15 19 ndime 11)
Sal. 32:8—Ndi mapindu otani amene timapeza tikamalandila malangizo ocokela kwa Yehova? (w09-CN 6/1 5 ndime 3)
Kodi kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwandiphunzitsa ciani za Yehova?
Ndi mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingagwilitsile nchito mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Salimo 32:1–33:8
KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) kt—Ŵelengani lemba pa cipangizo cokhala ndi intaneti.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Citani citsanzo coonetsa mmene tingayambitsile phunzilo la Baibulo kwa munthu amene timam’gaŵila magazini mwa kumuonetsa vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika pa Phunzilo la Baibulo? pa JW Laibulale.
Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) jl phunzilo 9—Mwacidule wofalitsa aonetse wophunzila mmene angagwilitsile nchito JW Laibulale pokonzekela misonkhano.
UMOYO WATHU WACIKRISTU
Zosoŵa za pampingo: (Mph. 15) Ngati mufuna, kambilanani zimene mwaphunzilapo pa nkhani za m’Buku Lapacaka. (yb16 masamba 112-113; ndi masamba 135-136)
Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu 16 ndime 16-29, bokosi pa tsa. 142, ndi kubwelelamo pa tsa. 144
Kubweleza Mfundo Zimene Taphunzila ndi Kufotokoza Zomwe Tidzaphunzila Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 16 ndi Pemphelo