SALIMO 26-33
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU |Dalilani Yehova Kuti Akulimbitseni Mtima
Kukumbukila mmene Yehova amapulumutsila kunalimbikitsa Davide
27:1-3
-
Yehova anapulumutsa Davide wacicepele ku mkango
-
Yehova anathandiza Davide kupha cimbalangondo kuti ateteze gulu la nkhosa
-
Yehova anathandiza Davide kupha Goliyati
N’ciani cingatithandize kukhala wolimba mtima ngati Davide?
27:4, 7, 11
-
Pemphelo
-
Kulalikila
-
Kupezeka pamisonkhano
-
Phunzilo laumwini ndi kulambila kwa pabanja
-
Kulimbikitsa ena
-
Kukumbukila mmene Yehova anatithandizila m’nthawi yakumbuyo