SALIMO 1-10
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU |Kuti Tikhale Pamtendele ndi Yehova, Tifunika Kulemekeza Mwana Wake, Yesu
Ulosi unakambilatu kuti anthu adzatsutsa ulamulilo wa Yehova ndi Yesu
2:1-3
-
Ulosi unakambilatu kuti anthu amitundu adzakana ulamulilo wa Yesu, koma adzafuna kumadzilamulila
-
Ulosi umenewu unakwanilitsidwa koyamba m’nthawi ya Yesu, ndipo masiku ano ukukwanilitsidwa pamlingo waukulu
-
Wamasalimo analemba kuti mitundu ya anthu ikung’ung’udza za cinthu copanda pake, kutanthauza kuti zolinga zao n’zopanda pake ndipo zidzalepheleka
Anthu amene amalemekeza Mfumu yodzozedwa ndi Yehova, ndiwo adzalandila moyo
2:8-12
-
Onse amene amatsutsa Mfumu Mesiya adzaonongedwa
-
Amene amalemekeza Mwana wa Mulungu, Yesu, ndi amene adzatetezedwa ndi kupeza mtendele