UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO May 2018
Makambilano Acitsanzo
Makambilano otsatizana-tsatizana okamba za tsogolo la anthu padziko lapansi.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Nyamula Mtengo Wako Wozunzikilapo na Kunditsatila Mosalekeza
N’cifukwa ciani tifunika kupemphela, kuŵelenga Baibo, kulalikila, na kusonkhana nthawi zonse?
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Thandizani Ana Anu Kuti Azitsatila Khristu
Kodi makolo angacite ciani kuti athandize ana awo kudzipeleka kwa Yehova Mulungu na kubatizika?
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Masomphenya Olimbitsa Cikhulupililo
Kodi masomphenya a cisanduliko anamukhudza bwanji Petulo? Kodi maulosi a m’Baibo angatikhudze bwanji?
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Cimene Mulungu Wacimanga Pamodzi . . . ”
Akhristu okwatilana amalemekeza kwambili malumbilo awo a cikwati. Amuna ndi Akazi angathane na mavuto mwa kutsatila mfundo za m’Baibo.
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Mkaziyo Anaponya Zambili Kuposa Ena Onse
Ni mfundo zofunika ziti zimene tiphunzilapo pa nkhani ya mkazi wamasiye amene anapeleka tundalama tuŵili tocepa mphamvu?
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Pewani Msampha wa Kuopa Anthu
N’cifukwa ciani atumwi anathaŵa zinthu zitavuta? Yesu ataukitsidwa, n’ciani cinathandiza atumwi kulalikila olo kuti anali kutsutsidwa?
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Yehova Adzakuthandiza Kukhala Wolimba Mtima
Kodi mumayopa kulalikila na kudziŵika kuti ndimwe wa Mboni za Yehova? Ngati n’conco, mungacite ciani kuti mukhale wolimba mtima polalikila za Yehova?