Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MALIKO 11–12

Mkaziyo Anaponya Zambili Kuposa Ena Onse

Mkaziyo Anaponya Zambili Kuposa Ena Onse

12:41-44

Kodi nkhani ya mkazi wamasiye ionetsa bwanji kuti. . . .

  • Yehova amayamikila zimene timacita?

  • tiyenela kucita zonse zimene tingathe potumikila Yehova?

  • sitifunika kumayelekezela zimene tingathe kucita na zimene ena amacita, olo na zimene kale tinali kukwanitsa kucita?

  • osauka afunika kupeleka zopeleka olo zitakhala zocepa?

Ni mfundo zinanso ziti zimene mwaphunzila?