Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

May 28–June 3

MALIKO 13-14

May 28–June 3
  • Nyimbo 55 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Pewani Msampha wa Kuopa Anthu”: (10 min.)

    • Maliko 14:29, 31—Atumwi analibe colinga cakuti am’kane Yesu

    • Maliko 14:50—Pamene Yesu anamangiwa, atumwi onse anathaŵa na kumusiya yekha

    • Maliko 14:47, 54, 66-72—Petulo analimba mtima poteteza Yesu, ndipo anamutsatila capatali, koma pambuyo pake anamukana katatu (ia peji 200 pala. 14; it-2 peji 619 pala. 6)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Maliko 14:51, 52—Kodi mnyamata amene anathaŵa ali malisece ayenela kuti anali ndani? (w08 2/15 peji 30 pala. 6)

    • Maliko 14:60-62—Kodi cifukwa cimene Yesu anayankhila funso la mkulu wa ansembe ciyenela kuti cinali ciani? (jy peji 287 pala. 4)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Maliko 14:43-59

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Itanilani munthuyo ku misonkhano.

  • Kubwelelako Kacitatu: (3 min. olo kucepelapo) Sankhani mwekha lemba. Ndipo gaŵilani cofalitsa cophunzitsila Baibo.

  • Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) bhs mape. 181-182 mapa. 17-18.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU