Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

May 7-13

MALIKO 7–8

May 7-13
  • Nyimbo 13 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Nyamula Mtengo Wako Wozunzikilapo ndi Kunditsatila Mosalekeza”: (10 min.)

    • Maliko 8:34—Kuti titsatile Khristu, tifunika kudzikana tekha (“adzikane yekhanwtsty mfundo younikila; w92 8/1 peji 17 pala. 14)

    • Maliko 8:35-37—Yesu anafunsa mafunso aŵili oticititsa kuganiza, amene angatithandize kuika maganizo athu pa zinthu zofunika kwambili (w08 10/15 mape. 25-26 mapa. 3-4)

    • Maliko 8:38—Kulimba mtima n’kofunika kuti titsatile Khristu (jy peji 143 pala. 4)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Maliko 7:5-8—N’cifukwa ciani kusamba m’manja kunali nkhani yaikulu kwa Afarisi? (w16.08 peji 30 mapa. 1-4)

    • Maliko 7:32-35—N’cifukwa ciani zimene Yesu anacita kwa munthu wogontha ni citsanzo cabwino kwa ise? (w00 2/15 mape. 17-18 mapa. 9-11)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Maliko 7:1-15

CITANI KHAMA PA ULALIKI

UMOYO WATHU WACIKHRISTU