June 14-20
DEUTERONOMO 5–6
Nyimbo 134 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Phunzitsani Ana Anu Kukonda Yehova”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Deut. 5:21—Kodi tiphunzilapo ciani pa lamulo loletsa kukhumbila mwansanje zinthu za ena? (w19.02 22 ¶11)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 5:1-21 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Pemphani mwininyumba kuti muziphunzila naye Baibo. Ndiyeno, chulani za vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (koma musaitambitse) (th phunzilo 9)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Sinthankoni ulaliki wanu kuti ugwilizane na zosoŵa za mwininyumba. Kenako ŵelengani lemba loyenelela. (th phunzilo 12)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) fg phunzilo 9 ¶6-7 (th phunzilo 8)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Onetsani Cikondi m’Banja”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Onetsani Cikondi Cosatha M’banja.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 41
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 148 na Pemphelo